Yohane 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komabe onse amene anamulandira,+ anawapatsa mphamvu zokhala ana a Mulungu,+ chifukwa amenewa anakhulupirira m’dzina lake.+ Aroma 8:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Onse amene akutsogoleredwa ndi mzimu wa Mulungu, amenewa ndiwo ana a Mulungu.+ 2 Akorinto 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Ndidzakhala atate wanu,+ ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi,’+ watero Yehova Wamphamvuyonse.”+
12 Komabe onse amene anamulandira,+ anawapatsa mphamvu zokhala ana a Mulungu,+ chifukwa amenewa anakhulupirira m’dzina lake.+
18 “‘Ndidzakhala atate wanu,+ ndipo inu mudzakhala ana anga aamuna ndi aakazi,’+ watero Yehova Wamphamvuyonse.”+