Levitiko 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake. Yeremiya 44:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndakukanani* ndipo ndikugwetserani tsoka ndi kupha anthu onse a mu Yuda.+ Ezekieli 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndidzamuyang’ana mokwiya+ n’kumuika kuti akhale chenjezo+ ndi mwambi.+ Ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu anga,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’+ Amosi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+
10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.
11 “Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndakukanani* ndipo ndikugwetserani tsoka ndi kupha anthu onse a mu Yuda.+
8 Ine ndidzamuyang’ana mokwiya+ n’kumuika kuti akhale chenjezo+ ndi mwambi.+ Ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu anga,+ ndipo anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’+
4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+