Levitiko 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndidzam’kana* munthu ameneyo, ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake,+ chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki kuti aipitse malo anga oyera+ ndi kuipitsa dzina langa loyera.+ Salimo 34:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+ Yeremiya 44:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndakukanani* ndipo ndikugwetserani tsoka ndi kupha anthu onse a mu Yuda.+ 1 Petulo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+
3 Ine ndidzam’kana* munthu ameneyo, ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake,+ chifukwa wapereka mwana wake kwa Moleki kuti aipitse malo anga oyera+ ndi kuipitsa dzina langa loyera.+
16 Nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa,+Kuti dzina lawo lisatchulidwenso padziko lapansi.+
11 “Choncho Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndakukanani* ndipo ndikugwetserani tsoka ndi kupha anthu onse a mu Yuda.+
12 Pakuti maso+ a Yehova* ali pa olungama, ndipo makutu ake amamva pembedzero lawo,+ koma nkhope ya Yehova imakwiyira anthu ochita zoipa.”+