Levitiko 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake. Levitiko 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 pamenepo ineyo ndidzam’kana munthu ameneyo pamodzi ndi banja lake,+ ndipo ndidzamupha pamodzi ndi onse ogwirizana naye pochita chiwerewere+ ndi Moleki, kuti asakhalenso pakati pa anthu awo. Yeremiya 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘“Mzinda uwu ndaukana* ndipo ukumana ndi tsoka osati zabwino,”+ watero Yehova. “Ndidzaupereka m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha ndi moto.”+ Amosi 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+
10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.
5 pamenepo ineyo ndidzam’kana munthu ameneyo pamodzi ndi banja lake,+ ndipo ndidzamupha pamodzi ndi onse ogwirizana naye pochita chiwerewere+ ndi Moleki, kuti asakhalenso pakati pa anthu awo.
10 “‘“Mzinda uwu ndaukana* ndipo ukumana ndi tsoka osati zabwino,”+ watero Yehova. “Ndidzaupereka m’manja mwa mfumu ya Babulo+ ndipo idzautentha ndi moto.”+
4 Akatengedwa ndi adani awo kupita ku ukapolo, kumeneko ndidzalamula lupanga kuti liwaphe.+ Ndidzakhala tcheru kuti ndiwagwetsere tsoka osati kuwapatsa madalitso.+