Ekisodo 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+ 1 Mafumu 20:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Tsopano mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza wamasula munthu woyenera kuwonongedwa ndi ine,+ moyo wako ulowa m’malo mwake+ ndipo anthu ako alowa m’malo mwa anthu ake.’”+
5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+
42 Tsopano mneneriyo anauza mfumuyo kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Popeza wamasula munthu woyenera kuwonongedwa ndi ine,+ moyo wako ulowa m’malo mwake+ ndipo anthu ako alowa m’malo mwa anthu ake.’”+