Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 6:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Pambuyo pake Beni-hadadi mfumu ya Siriya anasonkhanitsa asilikali ake onse ndipo anapita kukazungulira+ mzinda wa Samariya.

  • 2 Mafumu 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Hazaeli ataona zimenezi anafunsa kuti: “N’chifukwa chiyani mukulira mbuyanga?” Elisa anayankha kuti: “Chifukwa ndikudziwa bwino zoipa+ zimene iweyo udzachitire ana a Isiraeli. Malo awo otetezedwa udzawatentha ndi moto, amuna ochita kusankhidwa pakati pawo udzawapha ndi lupanga, ana awo aang’ono udzawaphwanyaphwanya,+ ndipo akazi awo apakati udzawatumbula.”+

  • 2 Mbiri 18:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika m’mapiri ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe atsogoleri.+ Aliyense abwerere kunyumba kwake mu mtendere.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena