Deuteronomo 28:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Chotero adzakuzungulirani m’mizinda yanu yonse kufikira mipanda yanu yaitali ndi yolimba kwambiri imene muzidzaidalira itagwa m’dziko lanu lonse. Adzakuzungulirani ndithu m’mizinda yanu yonse m’dziko lanu limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+ 1 Mafumu 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya anasonkhanitsa gulu lake lonse lankhondo ndiponso mahatchi+ ndi magaleta.+ Atatero ananyamuka pamodzi ndi mafumu ena 32,+ n’kupita kukazungulira+ mzinda wa Samariya+ kuti amenyane nawo.
52 Chotero adzakuzungulirani m’mizinda yanu yonse kufikira mipanda yanu yaitali ndi yolimba kwambiri imene muzidzaidalira itagwa m’dziko lanu lonse. Adzakuzungulirani ndithu m’mizinda yanu yonse m’dziko lanu limene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+
20 Beni-hadadi+ mfumu ya Siriya anasonkhanitsa gulu lake lonse lankhondo ndiponso mahatchi+ ndi magaleta.+ Atatero ananyamuka pamodzi ndi mafumu ena 32,+ n’kupita kukazungulira+ mzinda wa Samariya+ kuti amenyane nawo.