2 Mafumu 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pambuyo pake Beni-hadadi mfumu ya Siriya anasonkhanitsa asilikali ake onse ndipo anapita kukazungulira+ mzinda wa Samariya. 2 Mafumu 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno mfumu ya Asuri inabwera kudzachita nkhondo ndi dziko lonselo, kenako inazungulira mzinda wa Samariya+ kwa zaka zitatu.
24 Pambuyo pake Beni-hadadi mfumu ya Siriya anasonkhanitsa asilikali ake onse ndipo anapita kukazungulira+ mzinda wa Samariya.
5 Ndiyeno mfumu ya Asuri inabwera kudzachita nkhondo ndi dziko lonselo, kenako inazungulira mzinda wa Samariya+ kwa zaka zitatu.