Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma musadye+ nyama pamodzi ndi magazi+ ake, amene ndiwo moyo+ wake.

  • Levitiko 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘Musamadye mafuta kapena magazi+ alionse. Limeneli ndi lamulo ku mibadwo yanu yonse mpaka kalekale,* kulikonse kumene mungakhale.’”

  • Levitiko 7:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “‘Musamadye magazi+ alionse kulikonse kumene mungakhale, kaya akhale magazi a mbalame kapena a nyama.

  • Levitiko 19:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 “‘Musadye chilichonse limodzi ndi magazi.+

      “‘Musaombeze*+ ndipo musachite zamatsenga.+

  • Deuteronomo 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma musadye magazi ake.+ Muziwathira panthaka ngati madzi.+

  • 1 Samueli 14:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Tsopano anthu anauza Sauli kuti: “Taonani! Anthu akuchimwira Yehova mwa kudya nyama pamodzi ndi magazi ake.”+ Chotero iye anati: “Mwachita zinthu mosakhulupirika. Choyamba, kunkhunizani chimwala mubwere nacho kuno.”

  • Machitidwe 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena