Genesis 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma musadye+ nyama pamodzi ndi magazi+ ake, amene ndiwo moyo+ wake. Levitiko 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Musamadye magazi+ alionse kulikonse kumene mungakhale, kaya akhale magazi a mbalame kapena a nyama. Levitiko 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake. Deuteronomo 15:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma magazi ake okha usadye.+ Uziwathira pansi ngati madzi.+ 1 Samueli 14:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Tsopano anthu anauza Sauli kuti: “Taonani! Anthu akuchimwira Yehova mwa kudya nyama pamodzi ndi magazi ake.”+ Chotero iye anati: “Mwachita zinthu mosakhulupirika. Choyamba, kunkhunizani chimwala mubwere nacho kuno.” Ezekieli 33:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Choncho auze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu mumadya nyama limodzi ndi magazi ake,+ mumayang’anitsitsa mafano anu onyansa+ ndipo mumakhetsa magazi.+ Kodi pamenepa ndinu oyenera kutenga dzikoli kuti likhale lanu?+ Machitidwe 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”
26 “‘Musamadye magazi+ alionse kulikonse kumene mungakhale, kaya akhale magazi a mbalame kapena a nyama.
10 “‘Munthu aliyense wa nyumba ya Isiraeli kapena mlendo wokhala pakati panu, akadya magazi alionse,+ ndidzam’kana*+ ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu amtundu wake.
33 Tsopano anthu anauza Sauli kuti: “Taonani! Anthu akuchimwira Yehova mwa kudya nyama pamodzi ndi magazi ake.”+ Chotero iye anati: “Mwachita zinthu mosakhulupirika. Choyamba, kunkhunizani chimwala mubwere nacho kuno.”
25 “Choncho auze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Inu mumadya nyama limodzi ndi magazi ake,+ mumayang’anitsitsa mafano anu onyansa+ ndipo mumakhetsa magazi.+ Kodi pamenepa ndinu oyenera kutenga dzikoli kuti likhale lanu?+
29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”