Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma musadye+ nyama pamodzi ndi magazi+ ake, amene ndiwo moyo+ wake.

  • Levitiko 17:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 N’chifukwa chake ndauza ana a Isiraeli kuti: “Pasapezeke munthu wodya magazi ndipo pasapezeke mlendo wokhala pakati panu+ wodya magazi.”+

  • Deuteronomo 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma musadye magazi ake.+ Muziwathira panthaka ngati madzi.+

  • 1 Samueli 14:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Zitatero, anthuwo anayamba kuthamangira zofunkha mosusuka+ ndi kutenga nkhosa, ng’ombe ndi ana a ng’ombe. Zimenezi anali kuziphera pansi, ndipo anthuwo anayamba kudya nyamayo pamodzi ndi magazi ake.+

  • Machitidwe 15:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 kupitiriza kupewa zinthu zoperekedwa nsembe kwa mafano,+ magazi,+ zopotola,+ ndi dama.+ Mukamapewa zinthu zimenezi mosamala kwambiri,+ zinthu zidzakuyenderani bwino. Tikukufunirani zabwino zonse!”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena