Levitiko 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nʼchifukwa chake ndauza Aisiraeli kuti: “Aliyense wa inu asamadye magazi ndipo mlendo wokhala pakati panu+ asamadye magazi.”+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:12 Nsanja ya Olonda,6/15/2004, ptsa. 15-16
12 Nʼchifukwa chake ndauza Aisiraeli kuti: “Aliyense wa inu asamadye magazi ndipo mlendo wokhala pakati panu+ asamadye magazi.”+