Levitiko 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 N’chifukwa chake ndauza ana a Isiraeli kuti: “Pasapezeke munthu wodya magazi ndipo pasapezeke mlendo wokhala pakati panu+ wodya magazi.”+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:12 Nsanja ya Olonda,6/15/2004, ptsa. 15-16
12 N’chifukwa chake ndauza ana a Isiraeli kuti: “Pasapezeke munthu wodya magazi ndipo pasapezeke mlendo wokhala pakati panu+ wodya magazi.”+