Deuteronomo 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma musaphe akazi, ana aang’ono,+ ziweto+ ndi chilichonse chopezeka mumzindawo. Muzifunkha+ zinthu zonse za mumzindawo ndipo muzidya zimene mwafunkha kwa adani anu amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+ 1 Samueli 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiye n’chifukwa chiyani sunamvere mawu a Yehova, koma unathamangira zofunkha mosusuka+ ndi kuyamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova?”+
14 Koma musaphe akazi, ana aang’ono,+ ziweto+ ndi chilichonse chopezeka mumzindawo. Muzifunkha+ zinthu zonse za mumzindawo ndipo muzidya zimene mwafunkha kwa adani anu amene Yehova Mulungu wanu wakupatsani.+
19 Ndiye n’chifukwa chiyani sunamvere mawu a Yehova, koma unathamangira zofunkha mosusuka+ ndi kuyamba kuchita zinthu zoipa pamaso pa Yehova?”+