Numeri 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anatengera anthu ogwidwawo limodzi ndi zofunkha zina zonse kwa Mose, wansembe Eleazara, ndi kwa khamu la ana a Isiraeli. Anapita nawo kumsasa wawo ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+ Numeri 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zofunkhazo muzigawe pawiri. Hafu iperekedwe kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, ndipo hafu inayo iperekedwe kwa khamu la anthuwo.+ 2 Mbiri 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Asa ndi anthu amene anali naye anawathamangitsa mpaka kukafika ku Gerari,+ ndipo Aitiyopiyawo anapitiriza kuphedwa mpaka palibe amene anatsala ndi moyo, popeza Yehova+ ndi gulu lake+ anawagonjetseratu. Pambuyo pake, anthuwo anatenga zofunkha zochuluka zedi.+ Salimo 68:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mafumu enieniwo okhala ndi magulu a asilikali amathawa, ndithu amathawadi.+Mkazi wongokhala pakhomo, nayenso amagwira nawo ntchito yofunkha.+
12 Anatengera anthu ogwidwawo limodzi ndi zofunkha zina zonse kwa Mose, wansembe Eleazara, ndi kwa khamu la ana a Isiraeli. Anapita nawo kumsasa wawo ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, m’chipululu cha Mowabu.+
27 Zofunkhazo muzigawe pawiri. Hafu iperekedwe kwa asilikali omwe anapita kunkhondo, ndipo hafu inayo iperekedwe kwa khamu la anthuwo.+
13 Asa ndi anthu amene anali naye anawathamangitsa mpaka kukafika ku Gerari,+ ndipo Aitiyopiyawo anapitiriza kuphedwa mpaka palibe amene anatsala ndi moyo, popeza Yehova+ ndi gulu lake+ anawagonjetseratu. Pambuyo pake, anthuwo anatenga zofunkha zochuluka zedi.+
12 Mafumu enieniwo okhala ndi magulu a asilikali amathawa, ndithu amathawadi.+Mkazi wongokhala pakhomo, nayenso amagwira nawo ntchito yofunkha.+