Salimo 68:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mafumu okhala ndi magulu a asilikali amathawa,+ ndithu amathawadi. Mkazi amene amangokhala pakhomo, amalandira nawo zinthu zimene zalandidwa kunkhondo.+
12 Mafumu okhala ndi magulu a asilikali amathawa,+ ndithu amathawadi. Mkazi amene amangokhala pakhomo, amalandira nawo zinthu zimene zalandidwa kunkhondo.+