Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 31:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Anaphanso mafumu asanu achimidiyani.+ Mafumuwo anali Evi, Rekemu, Zuri, Hura ndi Reba. Komanso anapha Balamu+ mwana wa Beori ndi lupanga.

  • Yoswa 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma mafumu asanu aja anathawa+ n’kukabisala kuphanga la ku Makeda.+

  • Yoswa 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Yoswa ndi ana a Isiraeli anagonjetsa mafumu a kudera la kumadzulo kwa mtsinje wa Yorodano, kuchokera ku Baala-gadi+ kuchigwa cha Lebanoni+ mpaka kuphiri la Halaki,+ limene lili moyang’anizana ndi Seiri.+ Atawagonjetsa, Yoswa anapereka dzikolo kwa mafuko a Isiraeli poligawa m’magawomagawo.+

  • Oweruza 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mafumu anabwera ndi kumenya nkhondo.

      Pamenepo mafumu a Kanani anamenya nkhondo,+

      Anamenya nkhondo ku Taanaki,+ pafupi ndi madzi a ku Megido.+

      Iwo sanapezepo phindu la siliva.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena