Deuteronomo 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Adzapereka mafumu awo m’manja mwako,+ ndipo iwe udzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzaima kutsutsana ndi iwe+ kufikira utawafafaniza.+ Oweruza 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yomweyo, Sisera anasonkhanitsa magaleta ake onse ankhondo, magaleta 900 okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa m’mawilo.+ Anasonkhanitsanso anthu ake onse kuchokera ku Haroseti-ha-goimu, kupita kuchigwa cha Kisoni.+
24 Adzapereka mafumu awo m’manja mwako,+ ndipo iwe udzafafanize mayina awo padziko lapansi.+ Palibe munthu amene adzaima kutsutsana ndi iwe+ kufikira utawafafaniza.+
13 Nthawi yomweyo, Sisera anasonkhanitsa magaleta ake onse ankhondo, magaleta 900 okhala ndi zitsulo zazitali zakuthwa m’mawilo.+ Anasonkhanitsanso anthu ake onse kuchokera ku Haroseti-ha-goimu, kupita kuchigwa cha Kisoni.+