Oweruza 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ine ndidzakokera kwa iwe+ m’chigwa* cha Kisoni,+ Sisera+ mkulu wa gulu lankhondo la Yabini,+ pamodzi ndi magaleta ake ankhondo ndi gulu lake lonse. Pamenepo ndidzam’pereka m’manja mwako.’”+ Oweruza 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtsinje wa Kisoni unawakokolola,+Mtsinje wakalekale, mtsinje wa Kisoni.+Moyo wangawe, unapondereza adani amphamvu.+ Salimo 83:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+
7 Ine ndidzakokera kwa iwe+ m’chigwa* cha Kisoni,+ Sisera+ mkulu wa gulu lankhondo la Yabini,+ pamodzi ndi magaleta ake ankhondo ndi gulu lake lonse. Pamenepo ndidzam’pereka m’manja mwako.’”+
21 Mtsinje wa Kisoni unawakokolola,+Mtsinje wakalekale, mtsinje wa Kisoni.+Moyo wangawe, unapondereza adani amphamvu.+
9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+