1 Mafumu 18:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Gwirani aneneri a Baala! Muonetsetse kuti pasapezeke wothawa!” Nthawi yomweyo anawagwira, ndipo Eliya anatsetserekera nawo kuchigwa cha Kisoni,+ n’kukawapha kumeneko.+ Salimo 83:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+
40 Ndiyeno Eliya anauza anthuwo kuti: “Gwirani aneneri a Baala! Muonetsetse kuti pasapezeke wothawa!” Nthawi yomweyo anawagwira, ndipo Eliya anatsetserekera nawo kuchigwa cha Kisoni,+ n’kukawapha kumeneko.+
9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+