Oweruza 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mtsinje wa Kisoni unawakokolola,+Mtsinje wakalekale, mtsinje wa Kisoni.+Moyo wangawe, unapondereza adani amphamvu.+ Salimo 83:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+
21 Mtsinje wa Kisoni unawakokolola,+Mtsinje wakalekale, mtsinje wa Kisoni.+Moyo wangawe, unapondereza adani amphamvu.+
9 Muwachitire zimene munachitira Midiyani+ ndi Sisera.+Muwachitirenso zimene munachitira Yabini+ kuchigwa cha Kisoni.+