Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 31:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Amunawo anakathira nkhondo Amidiyani, monga mmene Yehova analamulira Mose, ndipo anapha mwamuna aliyense.+

  • Oweruza 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepa n’kuti Zeba ndi Zalimuna+ ali ku Karikori pamodzi ndi asilikali awo okwana pafupifupi 15,000. Asilikaliwa ndi amene anatsala pa gulu lonse la asilikali a Kum’mawa,+ ndipo amene anali ataphedwa anali asilikali 120,000.+

  • Yesaya 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti goli la katundu wawo,+ ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndiponso ndodo ya amene anali kuwakusira ku ntchito,+ mwazithyolathyola ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+

  • Yesaya 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Yehova wa makamu adzam’kwapula ndi chikwapu+ ngati mmene anagonjetsera Midiyani pathanthwe la Orebi.+ Ndodo yake idzakhala panyanja+ ndipo adzaikweza m’mwamba ngati mmene anachitira ndi Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena