Yesaya 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzamʼkwapula ndi chikwapu+ ngati mmene anachitira pamene anagonjetsa Midiyani pathanthwe la Orebi.+ Adzatambasula ndodo yake ndi kuloza panyanja ndipo adzaikweza mʼmwamba ngati mmene anachitira ndi Iguputo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:26 Yesaya 1, ptsa. 150-151
26 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba adzamʼkwapula ndi chikwapu+ ngati mmene anachitira pamene anagonjetsa Midiyani pathanthwe la Orebi.+ Adzatambasula ndodo yake ndi kuloza panyanja ndipo adzaikweza mʼmwamba ngati mmene anachitira ndi Iguputo.+