Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+

  • Yesaya 10:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “M’tsiku limenelo, katundu wake adzachoka paphewa panu,+ ndipo goli lake lidzachoka m’khosi mwanu.+ Golilo lidzathyoledwa+ chifukwa cha mafuta.”

  • Yeremiya 30:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Pa tsikuli ndidzathyola goli ndi kulichotsa m’khosi lanu. Ndidzadula zingwe zimene akumangani nazo,+ moti alendowo sadzagwiritsanso ntchito Yakobo monga wantchito wawo,” watero Yehova wa makamu.

  • Ezekieli 34:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Mtengo wam’munda udzabereka zipatso.+ Nthaka idzatulutsa zokolola zake.+ Iwo adzakhala m’dziko lawo mwabata.+ Ndikadzathyola goli lawo+ ndi kuwapulumutsa m’dzanja la amene anali kuwagwiritsa ntchito monga akapolo,+ adzadziwa kuti ine ndine Yehova.

  • Nahumu 1:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Tsopano ndidzathyola goli lake lonyamulira katundu ndi kulichotsa pa iwe,+ ndipo ndidzadula zingwe zimene anakumanga nazo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena