Yesaya 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzathyola Msuri amene ali m’dziko langa+ ndipo ndidzamupondaponda pamapiri anga.+ Goli lake lidzachoka pa iwo ndipo katundu wake adzachoka pamapewa awo.”+ Yeremiya 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Pa tsikuli ndidzathyola goli ndi kulichotsa m’khosi lanu. Ndidzadula zingwe zimene akumangani nazo,+ moti alendowo sadzagwiritsanso ntchito Yakobo monga wantchito wawo,” watero Yehova wa makamu. Hoseya 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinali kuwakoka mokoma mtima ndi mwachikondi,*+ moti kwa iwo ndinakhala ngati wochotsa goli m’khosi*+ mwawo ndipo mwachikondi ndinali kubweretsera aliyense wa iwo chakudya.+
25 Ndidzathyola Msuri amene ali m’dziko langa+ ndipo ndidzamupondaponda pamapiri anga.+ Goli lake lidzachoka pa iwo ndipo katundu wake adzachoka pamapewa awo.”+
8 “Pa tsikuli ndidzathyola goli ndi kulichotsa m’khosi lanu. Ndidzadula zingwe zimene akumangani nazo,+ moti alendowo sadzagwiritsanso ntchito Yakobo monga wantchito wawo,” watero Yehova wa makamu.
4 Ndinali kuwakoka mokoma mtima ndi mwachikondi,*+ moti kwa iwo ndinakhala ngati wochotsa goli m’khosi*+ mwawo ndipo mwachikondi ndinali kubweretsera aliyense wa iwo chakudya.+