Salimo 78:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.+Iye anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+ Salimo 105:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Anapempha nyama ndipo anawapatsa zinziri,+Anawadyetsa chakudya chochokera kumwamba.+
24 Ndipo anapitiriza kuwagwetsera mana ngati mvula kuti adye.+Iye anawapatsa tirigu wochokera kumwamba.+