2 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu. Yesaya 63:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+ Yohane 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Palibe munthu angabwere kwa ine akapanda kukokedwa ndi Atate amene anandituma ine,+ ndipo ine ndidzamuukitsa tsiku lomaliza.+
14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu.
9 Pamene iwo anali kuvutika m’masautso awo onse, iyenso anali kuvutika.+ Mthenga amene iye anawatumizira, anawapulumutsa.+ Chifukwa cha chikondi chake ndi chisoni chake, iye anawawombola.+ Anawakweza m’mwamba ndi kuwanyamula masiku onse akale.+
44 Palibe munthu angabwere kwa ine akapanda kukokedwa ndi Atate amene anandituma ine,+ ndipo ine ndidzamuukitsa tsiku lomaliza.+