1 Mbiri 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Sindidzachotsa kukoma mtima kwanga kosatha pa iye+ monga mmene ndinachitira kwa amene analipo iwe usanakhalepo.+ 1 Mbiri 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Kuwonjezera pamenepo, anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndiye adzamanga nyumba yanga+ ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndam’sankha kuti akhale mwana wanga+ ndipo ine ndidzakhala atate wake.+ Aheberi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako”?+ Kapena kuti: “Ine ndidzakhala atate wake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+
13 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Sindidzachotsa kukoma mtima kwanga kosatha pa iye+ monga mmene ndinachitira kwa amene analipo iwe usanakhalepo.+
6 “Kuwonjezera pamenepo, anandiuza kuti: ‘Mwana wako Solomo ndiye adzamanga nyumba yanga+ ndiponso mabwalo anga, chifukwa ndam’sankha kuti akhale mwana wanga+ ndipo ine ndidzakhala atate wake.+
5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako”?+ Kapena kuti: “Ine ndidzakhala atate wake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+