2 Samueli 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu. Salimo 89:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye amafuula kwa ine kuti, ‘Inu ndinu Atate wanga,+Mulungu wanga+ ndi Thanthwe la chipulumutso changa.’+ Aheberi 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako”?+ Kapena kuti: “Ine ndidzakhala atate wake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+
14 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Akachita zoipa, ine ndidzam’dzudzula ndi ndodo+ ya anthu ndi zikoti za ana a Adamu.
26 Iye amafuula kwa ine kuti, ‘Inu ndinu Atate wanga,+Mulungu wanga+ ndi Thanthwe la chipulumutso changa.’+
5 Mwachitsanzo, kodi Mulungu anauzapo mngelo uti kuti: “Iwe ndiwe mwana wanga. Lero ine ndakhala atate wako”?+ Kapena kuti: “Ine ndidzakhala atate wake ndipo iye adzakhala mwana wanga”?+