Salimo 89:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye adzafuula kwa ine kuti: ‘Inu ndinu Bambo anga,Mulungu wanga komanso Thanthwe la chipulumutso changa.’+
26 Iye adzafuula kwa ine kuti: ‘Inu ndinu Bambo anga,Mulungu wanga komanso Thanthwe la chipulumutso changa.’+