Salimo 89:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Iye amafuula kwa ine kuti, ‘Inu ndinu Atate wanga,+Mulungu wanga+ ndi Thanthwe la chipulumutso changa.’+
26 Iye amafuula kwa ine kuti, ‘Inu ndinu Atate wanga,+Mulungu wanga+ ndi Thanthwe la chipulumutso changa.’+