1 Samueli 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zitatero, Samueli anamuuza kuti: “Yehova wang’amba+ ndi kuchotsa ufumu wa Isiraeli kwa iwe lero, ndipo adzaupereka kwa mnzako, munthu woyenerera kuposa iwe.+ 1 Mbiri 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Sauli sanafunse kwa Yehova,+ chotero iye anamupha n’kupereka ufumuwo kwa Davide mwana wa Jese.+
28 Zitatero, Samueli anamuuza kuti: “Yehova wang’amba+ ndi kuchotsa ufumu wa Isiraeli kwa iwe lero, ndipo adzaupereka kwa mnzako, munthu woyenerera kuposa iwe.+