1 Mbiri 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Sindidzachotsa kukoma mtima kwanga kosatha pa iye+ monga mmene ndinachitira kwa amene analipo iwe usanakhalepo.+
13 Ine ndidzakhala atate wake+ ndipo iye adzakhala mwana wanga.+ Sindidzachotsa kukoma mtima kwanga kosatha pa iye+ monga mmene ndinachitira kwa amene analipo iwe usanakhalepo.+