Yesaya 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti goli la katundu wawo,+ ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndiponso ndodo ya amene anali kuwakusira ku ntchito,+ mwazithyolathyola ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+ Yesaya 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “M’tsiku limenelo, katundu wake adzachoka paphewa panu,+ ndipo goli lake lidzachoka m’khosi mwanu.+ Golilo lidzathyoledwa+ chifukwa cha mafuta.”
4 Pakuti goli la katundu wawo,+ ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndiponso ndodo ya amene anali kuwakusira ku ntchito,+ mwazithyolathyola ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+
27 “M’tsiku limenelo, katundu wake adzachoka paphewa panu,+ ndipo goli lake lidzachoka m’khosi mwanu.+ Golilo lidzathyoledwa+ chifukwa cha mafuta.”