Ekisodo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano Mose anatambasula dzanja lake kuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa mphepo yamphamvu yakum’mawa kuyamba kugawa nyanjayo usiku wonse ndi kuumitsa pansi pake.+ Motero madziwo anali kugawikana.+ Habakuku 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munadutsa panyanja ndi mahatchi anu, munadutsa pamadzi ambiri.+
21 Tsopano Mose anatambasula dzanja lake kuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa mphepo yamphamvu yakum’mawa kuyamba kugawa nyanjayo usiku wonse ndi kuumitsa pansi pake.+ Motero madziwo anali kugawikana.+