-
Salimo 136:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Yamikani amene anagawa pakati Nyanja Yofiira:+
Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
-