Ekisodo 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Choncho uwauze ana a Isiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndithu, ndidzakutulutsani mu Iguputo ndi kukuchotserani goli lawo, ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wawo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+ Ekisodo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala chete ngati mwala.Kufikira anthu anu+ atadutsa, inu Yehova,Kufikira anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+
6 “Choncho uwauze ana a Isiraeli kuti, ‘Ine ndine Yehova. Ndithu, ndidzakutulutsani mu Iguputo ndi kukuchotserani goli lawo, ndipo ndidzakulanditsani ku ukapolo wawo.+ Ndidzakuwombolani ndi dzanja langa lotambasula komanso ndi ziweruzo zamphamvu.+
16 Adzaopa ndipo adzagwidwa ndi mantha aakulu.+Chifukwa cha dzanja lanu lamphamvu, adzakhala chete ngati mwala.Kufikira anthu anu+ atadutsa, inu Yehova,Kufikira anthu anu amene munawapanga+ atadutsa.+