Yesaya 43:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Tsopano iwe Yakobo, mvera zimene wanena Yehova Mlengi wako,+ yemwe anakupanga+ iwe Isiraeli. Iye wanena kuti: “Usachite mantha, pakuti ine ndakuwombola.+ Ndakuitana pokutchula dzina.+ Iwe ndiwe wanga.+
43 Tsopano iwe Yakobo, mvera zimene wanena Yehova Mlengi wako,+ yemwe anakupanga+ iwe Isiraeli. Iye wanena kuti: “Usachite mantha, pakuti ine ndakuwombola.+ Ndakuitana pokutchula dzina.+ Iwe ndiwe wanga.+