Yesaya 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova, amene anakupanga+ ndiponso amene anakuumba,+ amene anali kukuthandiza ngakhale pamene unali m’mimba,+ wanena kuti, ‘Usachite mantha,+ iwe mtumiki wanga Yakobo, ndiponso iwe Yesuruni,+ amene ndakusankha. Yesaya 44:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Kumbukira zinthu zimenezi iwe Yakobo,+ ndiponso iwe Isiraeli, pakuti ndiwe mtumiki wanga.+ Ine ndiye amene ndinakuumba.+ Iweyo ndiwe mtumiki wanga. Iwe Isiraeli, ine sindikuiwala.+
2 Yehova, amene anakupanga+ ndiponso amene anakuumba,+ amene anali kukuthandiza ngakhale pamene unali m’mimba,+ wanena kuti, ‘Usachite mantha,+ iwe mtumiki wanga Yakobo, ndiponso iwe Yesuruni,+ amene ndakusankha.
21 “Kumbukira zinthu zimenezi iwe Yakobo,+ ndiponso iwe Isiraeli, pakuti ndiwe mtumiki wanga.+ Ine ndiye amene ndinakuumba.+ Iweyo ndiwe mtumiki wanga. Iwe Isiraeli, ine sindikuiwala.+