Yesaya 45:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chifukwa cha mtumiki wanga Yakobo ndi Isiraeli wosankhidwa wanga,+ ine ndinakuitana ndi dzina lako. Ndinakupatsa dzina laulemu, ngakhale kuti sunali kundidziwa.+
4 Chifukwa cha mtumiki wanga Yakobo ndi Isiraeli wosankhidwa wanga,+ ine ndinakuitana ndi dzina lako. Ndinakupatsa dzina laulemu, ngakhale kuti sunali kundidziwa.+