Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Yesaya 41:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+ iwe Yakobo amene ndakusankha,+ mbewu ya bwenzi langa+ Abulahamu.+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
8 “Koma iwe Isiraeli, ndiwe mtumiki wanga,+ iwe Yakobo amene ndakusankha,+ mbewu ya bwenzi langa+ Abulahamu.+