1 Mafumu 8:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Pakuti inuyo munawapatula pakati pa mitundu yonse ya anthu a padziko lapansi+ kuti akhale cholowa chanu, monga momwe munalankhulira kudzera mwa Mose+ mtumiki wanu, pamene munali kutulutsa makolo athu ku Iguputo, inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.” Salimo 135:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ya wadzisankhira Yakobo,+Wadzisankhira Isiraeli kukhala chuma chake chapadera.+
53 Pakuti inuyo munawapatula pakati pa mitundu yonse ya anthu a padziko lapansi+ kuti akhale cholowa chanu, monga momwe munalankhulira kudzera mwa Mose+ mtumiki wanu, pamene munali kutulutsa makolo athu ku Iguputo, inu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.”