Deuteronomo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti gawo la Yehova ndilo anthu ake.+Yakobo ndiye gawo la cholowa chake.+ Salimo 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+
12 Wodala ndi mtundu umene Mulungu wawo ndi Yehova,+Anthu amene iye wawasankha kukhala cholowa chake.+