Salimo 65:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+ Salimo 135:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ya wadzisankhira Yakobo,+Wadzisankhira Isiraeli kukhala chuma chake chapadera.+ 1 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma inu ndinu “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera,+ anthu odzakhala chuma chapadera,+ kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a amene anakuitanani kuchoka mu mdima kulowa m’kuwala kwake kodabwitsa.+
4 Wodala ndi munthu amene inu mwamusankha ndi kumuyandikizitsa kwa inu,+Kuti akhale m’mabwalo anu.+Tidzakhutira ndi zinthu zabwino za m’nyumba yanu,+Malo anu oyera kapena kuti kachisi wanu woyera.+
9 Koma inu ndinu “fuko losankhidwa mwapadera, ansembe achifumu, mtundu woyera,+ anthu odzakhala chuma chapadera,+ kuti mulengeze makhalidwe abwino kwambiri”+ a amene anakuitanani kuchoka mu mdima kulowa m’kuwala kwake kodabwitsa.+