1 Samueli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyale ya Mulungu inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona m’kachisi+ wa Yehova, mmene munali likasa la Mulungu. 1 Mbiri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+
3 Nyale ya Mulungu inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona m’kachisi+ wa Yehova, mmene munali likasa la Mulungu.
16 Motero analowetsa+ likasa la Mulungu woona muhema limene Davide anamanga, n’kuika likasalo pamalo ake muhemalo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zachiyanjano kwa Mulungu woona.+