Salimo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,+Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+ Salimo 84:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Odala ndi anthu amene akukhala m’nyumba yanu!+Iwo akupitirizabe kukutamandani.+ [Seʹlah.] Salimo 84:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti kukhala tsiku limodzi m’mabwalo anu n’kwabwino kuposa kukhala masiku 1,000 kwina.+Ndasankha kuima pakhomo la nyumba ya Mulungu wanga+Kuposa kukhala m’mahema a anthu oipa.+
4 Chinthu chimodzi chimene ndapempha kwa Yehova,+Chimenecho ndi chimene ndimachikhumba,+N’chakuti, ndikhale m’nyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,+Komanso kuti ndiyang’ane kachisi wake moyamikira.+
10 Pakuti kukhala tsiku limodzi m’mabwalo anu n’kwabwino kuposa kukhala masiku 1,000 kwina.+Ndasankha kuima pakhomo la nyumba ya Mulungu wanga+Kuposa kukhala m’mahema a anthu oipa.+