Salimo 84:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kukhala tsiku limodzi mʼmabwalo anu nʼkwabwino kuposa kukhala kwinakwake masiku 1,000!+ Ndasankha kuima pakhomo la nyumba ya Mulungu wangaKuposa kukhala mʼmatenti a anthu oipa. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 84:10 Nsanja ya Olonda,3/15/1997, tsa. 9
10 Kukhala tsiku limodzi mʼmabwalo anu nʼkwabwino kuposa kukhala kwinakwake masiku 1,000!+ Ndasankha kuima pakhomo la nyumba ya Mulungu wangaKuposa kukhala mʼmatenti a anthu oipa.