Salimo 84:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti kukhala tsiku limodzi m’mabwalo anu n’kwabwino kuposa kukhala masiku 1,000 kwina.+Ndasankha kuima pakhomo la nyumba ya Mulungu wanga+Kuposa kukhala m’mahema a anthu oipa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 84:10 Nsanja ya Olonda,3/15/1997, tsa. 9
10 Pakuti kukhala tsiku limodzi m’mabwalo anu n’kwabwino kuposa kukhala masiku 1,000 kwina.+Ndasankha kuima pakhomo la nyumba ya Mulungu wanga+Kuposa kukhala m’mahema a anthu oipa.+