1 Mbiri 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chiwerengero chawo, pamodzi ndi abale awo ophunzitsidwa kuimbira Yehova,+ onse akatswiri,+ chinakwana 288. Salimo 150:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 150 Tamandani Ya, anthu inu!+Tamandani Mulungu m’malo ake oyera.+Mutamandeni m’mlengalenga mmene mumasonyeza mphamvu zake.+
7 Chiwerengero chawo, pamodzi ndi abale awo ophunzitsidwa kuimbira Yehova,+ onse akatswiri,+ chinakwana 288.
150 Tamandani Ya, anthu inu!+Tamandani Mulungu m’malo ake oyera.+Mutamandeni m’mlengalenga mmene mumasonyeza mphamvu zake.+