1 Mbiri 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenaniya+ ndiye anali mtsogoleri wa Alevi pa ntchito yonyamula katundu, ndipo anali kupereka malangizo onyamulira katundu, chifukwa anali katswiri pa ntchito imeneyi.+
22 Kenaniya+ ndiye anali mtsogoleri wa Alevi pa ntchito yonyamula katundu, ndipo anali kupereka malangizo onyamulira katundu, chifukwa anali katswiri pa ntchito imeneyi.+